Ezekiel 4:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero chakudya ndi madzi zidzaŵathera pang'onopang'ono. Azidzada nkhaŵa akamapenyana, ndipo adzatheratu nkuwonda chifukwa cha machimo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti asowe chakudya ndi madzi, nasumwesumwe, naondetse mu mphulupulu zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzachita zimenezi kuti adzasowe chakudya ndi madzi. Choncho adzachita nkhawa akumapenyana ndipo adzatheratu ndi kuwonda chifukwa cha machimo awo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti asowe cakudya ndi madzi, nasumwesumwe, naondetse mu mphulupulu zao.