Ezekiel 40:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adapima chipata choloŵera. Chinali cha mamita asanu muufupi mwake. M'litali mwake chinali cha mamita 6 ndi theka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayesa kupingasa kwa chipata pakhoma pake mikono khumi, ndi utali wake wa chipata mikono khumi ndi itatu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anayeza chipata cholowera; mulifupi mwake munali mamita asanu ndipo mulitali mwake munali mamita asanu ndi limodzi ndi theka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anayesa kupingasa kwa cipata pakhoma pace mikono khumi, ndi utali wace wa cipata mikono khumi ndi itatu;