Ezekiel 40:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mseuwo unkayenda m'mphepete mwa zipata zija, molingana ndi kutalika kwake kwa zipatazo. Umenewu unali mseu wam'munsi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo moyalidwamo munali pa mbali ya zipata molingana ndi utali wake wa zipata, ndimo moyalidwa mwamunsi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Utali wa mulifupi mwa msewuwo unkayenda mamita 27 kufanana ndi utali wa chipata cholowera. Uwu unali msewu wa mʼmunsi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo moyalidwamo munali pa mbali ya zipata molingana ndi utali wace wa zipata, ndimo moyalidwa mwamunsi.