Ezekiel 40:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adayesa m'kati mwa bwalo kuchokera ku chipata cham'munsi mpaka ku chipata chakunja cha bwalo lam'kati. Kutalika kwake kunali mamita makumi asanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anayesa kupingasa kwake kuyambira pakhomo pake pachipata chakunsi, kufikira kumaso kwake kwa bwalo la m'kati kunja kwake, mikono zana kum'mawa, ndi kumpoto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono, anayeza kutalika kwa bwalo kuyambira chipata cholowera choyamba mpaka polowera pa chipata chakunja cha bwalo la mʼkati. Kutalika kwake kunali mamita makumi asanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anayesa kupingasa kwace kuyambira pakhomo pace pacipata cakunsi, kufikira kumaso kwace kwa bwalo la m'kati kunja kwace, mikono zana kum'mawa, ndi kumpoto.