Ezekiel 40:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati kutulo Chauta adapita nane ku dziko la Israele, nandiika pa phiri lalitali pamene ndidaona ngati mzinda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'masomphenya a Mulungu Iye anabwera nane m'dziko la Israele, nandikhalitsa pa phiri lalitali ndithu; pamenepo panali ngati mamangidwe a mudzi kumwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmasomphenyawo Yehova ananditenga ndi kupita nane ku dziko la Israeli ndipo anandiyika pa phiri lalitali kwambiri, moti ndinaona ngati mzinda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'masomphenya a Mulungu Iye anabwera nane m'dziko la Israyeli, nandikhalitsa pa phiri lalitali ndithu; pamenepo panali ngati mamangidwe a mudzi kumwela,