Ezekiel 40:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake munthuyo adayesa chipata chakumpoto chopitira ku bwalo lakunja. Adayesa m'litali mwake ndi muufupi mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi chipata cha bwalo lakunja choloza kumpoto anachiyesa m'litali mwake, ndi kupingasa kwake zonse mikono zana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka munthuyo anayeza mulitali ndi mulifupi mwa chipata chimene chimayangʼana kumpoto, chotulukira kunja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi cipata ca bwalo lakunja coloza kumpoto anaciyesa m'litali mwace, ndi kupingasa kwace.