Ezekiel 40:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwalo lam'kati linali ndi khomo loyang'ana kumwera. Adaliyesa kuchokera ku chipata chimenechi mpaka ku chipata chakunja, kutalika kwake kunali mamita makumi asanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali chipata cha bwalo lam'kati chakuloza kumwera, nayesa kuyambira kuchipata kufikira kuchipata kumwera mikono zana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bwalo lamʼkati linalinso ndi chipata kummwera. Munthuyo analiyeza kuchokera ku chipata chimenechi mpaka ku chipata chakunja. Kutalika kwake kunali mamita makumi asanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali cipata ca bwalo lam'kati cakulozakumwela, nayesa kuyambira kucipata kufikira kucipata kumwela mikono zana.