Ezekiel 40:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono panali makonde pozungulira ponse. Lililonse m'litali mwake munali mamita 12 ndi theka, muufupi mwake mamita aŵiri ndi theka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali zidundumwa pozungulirapo, m'litali mwake mikono makumi awiri mphambu isanu, ndi kupingasa kwake mikono isanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Khonde lililonse la makonde atatu a zipata zolowera bwalo lamʼkati aja linali la mamita ozungulira mʼbwalo lamʼkati anali mamita 13 mulitali mwake, mamita awiri ndi theka mulifupi mwake).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali zidundumwa pozungulirapo, m'litali mwace mikono makumi awiri mphambu isanu, ndi kupingasa kwace mikono isanu.