Ezekiel 40:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka munthuyo adapita nane m'bwalo lam'kati chakuvuma. Adachiyesa chipatacho napeza kuti chinali cholingana ndi zinzake zina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analowa ndine m'bwalo lam'kati kuloza kum'mawa, nayesa chipata cha kum'mawa monga mwa miyeso yomweyi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka munthuyo anapita nane ku bwalo la mʼkati mbali ya kummawa, ndipo anayeza chipata cholowera; chinali chofanana ndi zinzake zina zija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analowa ndine m'bwalo lam'kati kuloza kum'mawa, nayesa cipata ca kum'mawa monga mwa miyeso yomweyi;