Ezekiel 40:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adapita nane ku chipata chakumpoto. Adachiyesa napeza kuti ncholingana ndi zinzake zija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anabwera nane kuchipata cha kumpoto, nachiyesa monga mwa miyeso yomweyi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anapita nane ku chipata chakumpoto ndipo anachiyeza. Chinali chofanana ndi zina zija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anabwera nane ku cipata ca kumpoto, naciyesa monga mwa miyeso yomweyi;