Ezekiel 40:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adandiwuza kuti, “Chipinda choyang'ana kumwerachi ncha ansembe oyang'anira Nyumba ya Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa ine, Kanyumba aka koloza kumwera nka ansembe odikira Kachisi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthuyo anandiwuza kuti, “Chipinda chimene chikuyangʼana kummwera ndi cha ansembe amene amayangʼanira Nyumba ya Mulungu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa ine, Kanyumba aka koloza kumwela nka ansembe odikira kacisi.