Ezekiel 40:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapita ku chipata choyang'ana kuvuma, adakwera pa makwerero ake napima chiwundo cha pachipatapo, kutalika kwake kunali bango lathunthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anafika kuchipata choloza kum'mawa, nakwera pa makwerero ake; ndipo anayesa chiundo cha chipata, bango limodzi kuchindikira kwake; ndicho chiundo choyamba, bango limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapita ku chipata chakummawa. Anakwera pa makwerero a nyumbayo, nayeza chiwundo choyamba cha chipatacho; kutalika kwake kunali mamita atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anafika ku cipata coloza kum'mawa, nakwera pa makwerero ace; ndipo anayesa ciundo ca cipata, bango limodzi kucindikira kwace; ndico ciundo coyamba, bango limodzi.