Ezekiel 40:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapima khonde lam'kati lapachipata, napeza kuti linali la mamita anai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anayesanso khonde la kuchipata kumbali ya ku Kachisi, bango limodzi. Pamenepo anayesa khonde la kuchipata mikono isanu ndi itatu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iye anayeza khonde la chipata ndipo chinali cha mamita atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anayesanso khonde la kucipata ku mbali ya kukacisi, bango limodzi.