Ezekiel 41:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndi zipinda za Nyumba ya Mulunguyo panali bwalo la mamita khumi m'kupingasa kwake, kuzungulira Nyumba yonseyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pakati pa zipinda panali kupingasa kwa mikono makumi awiri, pozungulira pake ponse pa nyumba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi zipinda za Nyumba ya Mulungu panali bwalo limeneli la mamita khumi kupingasa kwake kuzungulira Nyumba yonse ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pakati pa zipinda panali kupingasa kwa mikono makumi awiri, pozungulira pace ponse pa nyumba.