Ezekiel 41:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono munthu uja adayesa Nyumba ya Mulungu, m'litali mwake inali ya mamita makumi asanu. Bwalo la Nyumbayo ndi makoma ake, zonse zinali za mamita makumi asanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo anayesa Kachisi m'litali mwake mikono zana limodzi; ndi mpatawo, ndi nyumbayo, ndi makoma ake, mikono zana limodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo munthuyo anayeza Nyumba ya Mulungu ndipo mulitali mwake inali mamita makumi asanu. Nyumbayo ndi makoma ake, zonse zinali za mamita makumi asanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo anayesa kacisi m'litali mwace mikono zana limodzi; ndi mpatawo, ndi nyumbayo, ndi makoma ace, mikono zana limodzi;