Ezekiel 41:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumaso kwa Nyumba ya Mulungu chakuvuma kwa bwalolo muufupi mwake munali mamita makumi asanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kupingasa kwake komwe kwa kukhomo kwa nyumba, ndi kumpatawo kum'mawa, mikono zana limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumaso kwa Nyumba ya Mulungu chakummawa kwa bwalolo mulifupi mwake munali mamita makumi asanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kupingasa kwace komwe kwa kukhomo kwa nyumba, ndi ku mpatawo kum'mawa, mikono zana limodzi.