Ezekiel 41:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamwamba pa khomo loloŵera ku chipinda cham'kati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kufikira kumwamba pa khomo, mpaka nyumba ya m'katimo, ndi kunja kwake, ndi khoma lonse kwete m'kati ndi kunja, monga mwa miyeso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamwamba pa khomo lolowera ku malo opatulika amʼkati komanso kuzungulira makoma onse kunja ndi mʼkati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kufikira pamwamba pa khomo, mpaka nyumba ya m'katimo, ndi kunja kwace, ndi khoma lonse kwete m'kati ndi kunja, monga mwa miyeso.