Ezekiel 41:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mphuthu za chipinda cham'thunthu kutalika kwake mbali zonse kunali kolingana. Kumaso kwa malo opatulika kunali chinthu chooneka ngati
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mphuthu za Kachisi zinali zaphwamphwa, ndi maonekedwe a pakhomo pa malo opatulika ananga maonekedwe a Kachisi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mphuthu za chipinda chachikulu cha Nyumba ya Mulungu kutalika kwake mbali zonse kunali kofanana. Ndipo kumaso kwa malo opatulika kunali chinthu china chooneka ngati
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mphuthu za Kacisi zinali zamphwamphwa, ndi maonekedwe a pakhomo pa malo opatulika ananga maonekedwe a kacisi.