Ezekiel 41:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pazitsekopo adazokotapo zithunzi za akerubi ndi za kanjedza, monga pa makoma aja. Kunja kwake kunali ngati denga lamatabwa pamwamba pa khonde lam'kati.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panalembedwa pamenepo pa zitseko za Kachisi akerubi ndi akanjedza, akunga aja adalembedwa pamakoma; ndipo panali matabwa ochindikira pakhomo pakhonde panja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pa zitsekopo anajambulipo zithunzi za akerubi ndi kanjedza monga zomwe anajambulapo pa makoma. Kunja kwake kunali ngati denga lamatabwa pamwamba pa khonde lamʼkati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panalembedwa pamenepo pa Izitseko za Kacisi akerubi ndi akanjedza, akunga aja adalembedwa pamakhoma; ndipo panali matabwa ocindikira pakhomo pakhonde panja,