Ezekiel 41:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Khoma la kunja kwa zipindazo linali la mamita aŵiri ndi theka kuchindikira kwake. Pakati pa chiwundocho
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuchindikira kwa khoma la kuzipinda za m'mphepete kunja kwake kunali mikono isanu; ndipo mpata wake unali malo olowera m'zipinda za m'mphepete za Kachisi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Khoma lakunja la zipindazo linali la mamita awiri ndi theka kuchindikira kwake. Pakati pa chiwundocho
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kucindikira kwa khoma la kuzipinda za m'mphepete kunja kwace kunali mikono isanu; ndipo mpata wace unali malo olowera m'zipinda za m'mphepete za kacisi.