Ezekiel 42:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adayesa mbali yakuvuma ndi bango loyesera lija, kutalika kwake kunali kwa mamita 250.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anayesa mbali ya kum'mawa, ndi bango loyesera, mikono mazana asanu, kuyesa ndi bango loyesera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anayeza mbali yakummawa ndi ndodo yake yoyezera; kutalika kwake kunali mamita 250.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anayesa mbali ya kum'mawa ndi bango loyesera, mabango mazana asanu, kuyesa ndi bango loyesera, pozungulira pace.