Ezekiel 42:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adatembenuka nayesa mbali yakumpoto ndi bango lakelo, kutalika kwake kunali kwa mamita 250.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anayesa mbali ya kumpoto mikono mazana asanu, kuyesa ndi bango loyesera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anayeza mbali ya kumpoto ndi ndodo yake; kutalika kwake kunali mamita 250.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anayesa mbali ya kumpoto mabango mazana asanu, kuyesa ndi bango loyesera, pozungulira pace.