Ezekiel 42:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatembenuka nayesa mbali yakumwera ndi bango lake. Kutalika kwake kunali kwa mamita 250.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anayesa mbali ya kumwera mikono mazana asanu, kuyesa ndi bango loyesera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthuyo anayeza mbali yakummwera; kutalika kwake kunali mamita 250 atayeza ndi ndodo yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anayesa mbali ya kumwela mabango mazana asanu, kuyesa ndi bango loyesera,