Ezekiel 42:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatembenukanso nayesa kuzambwe ndi bango lake. Kutalika kwake kunali kwa mamita 250.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anatembenukira kumbali ya kumadzulo, nayesa mikono mazana asanu ndi bango loyesera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anatembenukira ku mbali ya kumadzulo ndi kuyeza ndi ndodo yake; kutalika kwake kunali mamita 250 atayeza ndi ndodo yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anatembenukira ku mbali ya kumadzulo, nayesa mabango mazana asanu ndi bango loyesera.