Ezekiel 42:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyumba yakumpotoyi m'litali mwake inali ya mamita makumi asanu, muufupi mwake inali ya mamita 25.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chakuno cha m'litali mwake mwa mikono zana limodzi kunali khomo la kumpoto, ndi kupingasa kwake mikono makumi asanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyumba yakumpotoyi mulitali mwake munali mamita makumi asanu, mulifupi mwake munali mamita 25.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cakuno ca m'litali mwace mwa mikono zana limodzi kunali khomo la kumpoto, ndi kupingasa kwace mikono makumi asanu.