Ezekiel 42:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pansi pa zipinda zimenezi panali khoma lake chakuvuma, kuchokera ku bwalo lakunja kumene khoma la bwalo linkayambira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pansi pa zipinda izi panali polowera mbali ya kum'mawa, poloweramo kuchoka kubwalo lakunja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pansi pa zipinda zimenezi panali khomo chakummawa kuchokera ku bwalo lakunja kumene khoma lake linkayambira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pansi pa zipinda izi panali polowera mbali ya kum'mawa, poloweramo kucoka ku bwalo lakunja.