Ezekiel 43:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malo osonkhapo moto pa guwa msinkhu wake udzakhala mamita aŵiri. Pamwamba pake padzatuluka nyanga zinai, kutalika kwake theka la mita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi guwa lapamwamba mikono inai; ndi pamoto pa guwa padzatuluka nyanga zinai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malo osonkhapo moto pa guwa, msinkhu wake udzakhala mamita awiri. Pa ngodya iliyonse ya malo osonkhapo motowo panatuluka nyanga imodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi guwa lapamwamba mikono inai; ndi pamoto pa guwa padzaturuka nyanga zinai.