Ezekiel 43:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malo osonkhapo motowo kutalika kwake kudzakhala mamita asanu ndi limodzi, muufupi mwakenso mamita asanu ndi limodzi, motero adzakhala olingana mbali zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pamoto pa guwa, m'litali mwake mikono khumi ndi iwiri, ndi kupingasa kwake khumi ndi iwiri, laphwamphwa mbali zake zinai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malo osankhalapo moto pa guwa lansembe miyeso yake ndi yofanana mbali zonse. Mulitali mwake mudzakhala mamita asanu ndi limodzi ndipo mulifupi mwake mudzakhalanso mamita asanu ndi limodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pamoto pa guwa, m'litali mwace mikono khumi ndi iwiri, ndi kupingasa kwace khumi ndi iwiri, lampwamphwa mbali zace zinai.