Ezekiel 43:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Masiku asanu ndi aŵiriwo adzachite mwambo wopepesera milandu ndi kuyeretsa guwa, kuti alipatulire Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku asanu ndi awiri achite chotetezera guwali ndi kuliyeretsa, momwemo alipatule.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa masiku asanu ndi awiriwo ansembe adzachite mwambo woyeretsa ndi kupatula guwa lansembelo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku asanu ndi awiri acite cotetezera guwali ndi kuliyeretsa, momwemo alipatule.