Ezekiel 43:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mzimu wa Mulungu udandinyamula numandiloŵetsa m'bwalo lam'kati. Ndipo ulemerero wa Chauta udadzaza Nyumba yakeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mzimu unandinyamula numuka nane kubwalo la m'kati; ndipo taonani, ulemerero wa Yehova unadzaza Kachisi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Mzimu unandinyamula nundilowetsa mʼbwalo lamʼkati, ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza Nyumba ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mzimu unandinyamula numuka nane ku bwalo la m'kati; ndipo taonani, ulemerero wa Mulungu unadzaza kacisi.