Ezekiel 43:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu uja ataima pambali panga, ndidamva wina akundilankhula kuchokera m'Nyumba ya Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinamva wina alikulankhula nane ali m'Kachisi, naima nane munthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthuyo ali chiyimire pambali panga, ndinamva wina akundiyankhula kuchokera mʼNyumba ya Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinamva wina alikulankhula nane ali m'kacisi, naima nane munthu.