Ezekiel 44:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu uja adapita nane ku chipata cha kunja kwa malo opatulika choyang'ana kuvuma. Chinali chotseka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anandibweza njira ya kuchipata chakunja cha malo opatulika choloza kum'mawa, koma chinatsekedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu uja anabwerera nane ku chipata chakunja kwa malo opatulika, chomwe chimayangʼana kummawa. Chipatacho chinali chotseka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anandibweza njira ya ku cipata cakunja ca malo opatulika coloza kum'mawa, koma cinatsekedwa.