Ezekiel 44:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe ndidzaŵaika kuti aziyang'anira Nyumba yanga ndi kutumikira pa ntchito zonse zoyenera kuchitika kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndidzawaika akhale osunga udikiro wa Kachisi kwa utumiki wake wonse, ndi zonse zakumachitika m'mwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe ndidzawayika kuti aziyangʼanira Nyumba yanga ndi kutumikira pa ntchito zake zonse zoyenera kuti zigwiridwe mʼmenemo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndidzawaika akhale osunga udikiro wa kacisi kwa utumiki wace wonse, ndi zonse zakumacitika m'mwemo.