Ezekiel 44:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo okhawo ndiwo adzaloŵe ku malo anga opatulika ndi kudzayandikira tebulo langa kuti anditumikire. Ndiwo amene adzasamalire zinthu zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
iwowa adzalowa m'malo anga opatulika, nadzayandikira kugome langa kunditumikira, nadzasunga udikiro wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Okhawa ndiwo adzalowe ku malo anga opatulika ndi kudzayandikira tebulo langa kuti adzanditumikire. Amenewa okha ndiwo adzasamalire zinthu zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
iwowa adzalowa m'malo anga opatulika, nadzayandikira ku gome langa kunditumikira, nadzasunga udikiro wanga.