Ezekiel 44:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kalonga yekha angathe kukhala pamenepo ndi kumadya chakudya pamaso pa Chauta. Adzaloŵa ndi kutuluka kudzera m'khonde lam'kati la chipata chimenecho.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kunena za kalonga, iye akhale m'menemo monga kalonga kudya mkate pamaso pa Yehova; alowe kunjira ya kukhonde la chipata, natulukire njira yomweyi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kalonga yekha angathe kukhala mʼmenemo ndi kumadya chakudya pamaso pa Yehova. Iye adzalowere pa njira ya ku khonde lamʼkati ndi kutulukiranso njira yomweyo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kunena za kalonga, iye akhale m'menemo monga kalonga kudya mkate pamaso pa Yehova; alowe ku njira ya ku khonde la cipata, naturukire njira yomweyi.