Ezekiel 44:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kaya ndi mbalame kaya ndi nyama, ansembe asadye yofa yokha kapena yochita kujiwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ansembe asadyeko kanthu kakufa kokha, kapena kogwidwa ndi chilombo, ngakhale mbalame, kapena nyama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ansembe sayenera kudya kalikonse kofa kokha, kaya mbalame, kapena nyama. Kapena yochita kujiwa.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ansembe asadyeko kanthu kakufa kokha, kapena kogwidwa ndi cirombo, ngakhale mbalame, kapena nyama.