Ezekiel 44:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a mtundu waupandu wa Israele uŵauze mau anga akuti, Aisraele inu, lekani zonyansa zanu zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nunene kwa opandukawo, kwa nyumba ya Israele, Atero Ambuye Yehova, Nyumba ya Israele inu, Zikukoleni zonyansa zanu zonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uwuze mtundu wopanduka wa Israeli kuti Ine Ambuye Yehova ndikuti: Inu Aisraeli, andikwana machitidwe anu onyansawo!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nunene kwa opandukawo, kwa nyumba ya Israyeli, Atero Ambuye Yehova, Nyumba ya Israyeli inu, Zikukoleni zonyansa zanu zonse;