Ezekiel 44:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'malo moti muzisamala ndinu zinthu zanga zopatulika, mwasankha alendoŵa kuti aziyang'anira malo anga opatulika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo simunasunga udikiro wa zopatulika zanga, koma mwadziikira mokha osunga udikiro wanga m'malo anga opatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmalo moti muzisamalira zinthu zanga zopatulika, mwayika alendo kuti aziyangʼanira malo anga opatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo simunasunga udikiro wa zopatulika zanga, koma mwadziikira mokha osunga udikiro wanga m'malo anga opatulika.