Ezekiel 45:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Miyeso yanu yoyesera zinthu monga efa ndi bati, izikhala yokhulupirika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muzikhala nayo miyeso yoona, ndi efa woona, ndi bati loona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Miyeso yanu yoyezera zinthu monga efa ndi bati zizikhala zokhulupirika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muzikhala nayo miyeso yoona, ndi efa woona, ndi bati loona.