Ezekiel 45:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiponso chimodzi mwa zigawo 100 za mafuta. Miyeso yake ili motere: mabati khumi alingana ndi homeri imodzi kapena kori imodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi gawo lonenedwa la mafuta, la bati wa mafuta, ndilo limodzi la magawo khumi la bati, kulitapa pa kori; ndiwo mabati khumi, ndiwo homeri; pakuti mabati khumi ndiwo homeri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gawo loyenera la mafuta, loyezedwa ndi bati, ndiponso chigawo mwa zigawo 100 za mafuta. Miyeso yake ili motere: mabati khumi afanana ndi homeri imodzi kapena kori imodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi gawo lonenedwa la mafuta, la bati wa mafuta, ndilo limodzi la magawo khumi la bati, kulitapa pa kori; ndiwo mabati khumi, ndiwo homeri; pakuti mabati khumi ndiwo homeri;