Ezekiel 45:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku loyamba la chikondwererocho, mfumu ipereke nsembe ya ng'ombe yamphongo kupepesera machimo ake ndiponso a anthu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsiku lomwelo kalonga adzikonzere yekha ndi anthu onse a m'dziko ng'ombe, ikhale ya nsembe yauchimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku loyamba la chikondwererocho, mfumu ipereke nsembe ya ngʼombe yayimuna monga nsembe yopepesera machimo ake ndi machimo a anthu onse a mʼdziko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsiku lomwelo kalonga adzikonzere yekha ndi anthu onse a m'dziko ng'ombe, ikhale ya nsembe yaucimo.