Ezekiel 45:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamodzi ndi ng'ombe iliyonse yamphongo ndi nkhosa iliyonse yamphongo, mfumu ipereke chopereka cha zakudya chokwanira efa imodzi ndiponso ya mafuta okwanira hini imodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakonze nsembe yaufa, kung'ombe kukhale efa; ndi kunkhosa yamphongo kukhale efa; ndi kuefa kukhale hini wa mafuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamodzi ndi ngʼombe iliyonse yayimuna ndi nkhosa iliyonse yayimuna, mfumu ipereke chopereka cha chakudya chokwanira efa imodzi ndiponso mafuta okwanira hini imodzi pa efa iliyonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakonze nsembe yaufa, ku ng'ombe kukhale efa; ndi ku nkhosa yamphongo kukhale efa; ndi kuefa kukhale hini wa mafuta.