Ezekiel 46:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero azipereka mwanawankhosa, ufa ndi mafuta m'maŵa mulimonse, kuti zikhale zopsereza tsiku ndi tsiku.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo apereke mwanawankhosa, ndi nsembe yaufa, ndi mafuta, m'mawa ndi m'mawa, nsembe yopsereza kosalekeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero azipereka mwana wankhosa ndi chopereka cha chakudya ndi mafuta mmawa uliwonse kuti zikhale nsembe zopsereza za tsiku ndi tsiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo apereke mwana wa nkhosa, ndi nsembe yaufa, ndi mafuta, m'mawa ndi m'mawa, nsembe yopsereza kosalekeza.