Ezekiel 46:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adandiwuza kuti, “Zimenezi ndizo zipinda zophikiramo, kumene anthu otumikira m'Nyumba ya Mulungu aziphikiramo nyama za nsembe za anthu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa ine, Izi ndi nyumba zophikiramo, kumene atumiki a Kachisi aziphikira nsembe ya anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthuyo anandiwuza kuti, “Izi ndi zipinda zophikiramo. Mʼmenemu anthu otumikira ku Nyumba ya Mulungu adzaphikiramo nyama za nsembe za anthu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa ine, Izi ndi nyumba zophikiramo, kumene atumiki a kacisi aziphikira nsembe ya anthu.