Ezekiel 46:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu nawonso azipembedza pamaso pa Chauta pa khomo la chipata chimenecho pa masiku a Sabata ndiponso pa tsiku limene mwezi wakhala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu a m'dziko alambire pa chitseko cha chipata ichi pamaso pa Yehova pamasabata, ndi pokhala mwezi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a mʼdziko azipembedza pamaso pa Yehova pa khomo la chipata chimenechi pa masiku a sabata ndi pa tsiku la mwezi watsopano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu a m'dziko alambire pa citseko ca cipata ici pamaso pa Yehova pamasabata, ndi pokhala mwezi.