Ezekiel 47:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Berata ndi Sibraimu, mizinda imene ili pakati pa malire a Damasiko ndi Hamati, mpaka ku Hazere-Hatikoni pafupi ndi malire a Haurani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Hamati, Berota, Sibraimu, ndiwo pakati pa malire a Damasiko, ndi malire a Hamati; Hazere-Hatikoni ndiwo kumalire a Haurani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Berota ndi Sibraimu (mizinda imene ili pakati pa malire a Damasiko ndi Hamati mpaka kukafika ku Hazeri Hatikoni mzinda umene uli mʼmalire mwa Haurani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Hamati, Berota, Sibraimu, ndiwo pakati pa malire a Damasiko, ndi malire a Hamati; Hazere Hatikoni ndiwo ku malire a Haurani.