Ezekiel 47:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Malire akuzambwe akhale Nyanja Yaikulu mpaka ku malo oyang'anana ndi chipata cha Hamati. Imeneyi ndiyo mbali yakuzambwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mbali ya kumadzulo ndiyo Nyanja Yaikulu, kuyambira malire a kumwera kufikira pandunji polowera ku Hamati. Ndiyo mbali ya kumadzulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbali ya kumadzulo, malire adzakhala Nyanja Yayikulu mpaka pa malo oyangʼanana ndi Lebo Hamati. Awa adzakhala malire akumadzulo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mbali ya kumadzulo ndiyo nyanja yaikuru, kuyambira malire a kumwela kufikira pandunji polowera ku Hamati. Ndiyo mbali ya kumadzulo.