Ezekiel 47:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo adandiwuza kuti, “Iwe mwana wa munthu, waziwonatu zimenezi ati?” Atatero adandibwezera ku gombe la mtsinjewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, waona ichi? Nanditenga kundikwezetsa ndi mtsinje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthuyo anandifunsa kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi ukuziona zimenezi?” Kenaka anabwerera nane ku gombe la mtsinjewo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, waona ici? Nanditenga kundikwezetsa ndi mtsinje.