Ezekiel 47:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono munthuyo adandiwuza kuti, “Madzi ameneŵa akupita ku chigawo chakuvuma cha dziko kutsikira ku chigwa cha Araba. Potsiriza pake, akakathira m'Nyanja Yakufa imene madzi ake ali oipa, madziwo adzakoma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anati kwa ine, Madzi awa atulukira kudera la kum'mawa, natsikira kuchidikha, nayenda kunyanja; atathira kunyanja akonzeka madzi ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono munthuyo anandiwuza kuti, “Madziwa akupita ku chigawo chakummawa ndi kutsikira ku chigwa cha Araba. Kenaka akathira mʼNyanja Yakufa, ndipo akakalowa mʼnyanjayo, madzi a nyanjayo adzasanduka okoma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anati kwa ine, Madzi awa aturukira ku dera la kum'mawa, natsikira kucidikha, nayenda kunyanja; atathira kunyanja akonzeka madzi ace.