Ezekiel 48:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Asagulitse kapena kusinthitsa mbali iliyonse ya chigawo chimenechi. Ndi chigawo chapadera ndithu ndipo asachipatse ena, pakuti ndi malo opatulikira Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo asagulitseko, kapena kulisintha, kapena kupitiriza zipatso zoyamba za dziko; pakuti lili lopatulika la Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asagulitse kapena kusinthitsa mbali iliyonse ya chigawo chimenechi. Ichi ndi chigawo chabwino kwambiri ndipo chisapatsidwe kwa anthu ena, chifukwa ndi chopatulikira Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo asagulitseko, kapena kulisintha, kapena kupitiriza zipatso zoyamba za dziko; pakuti liri lopatulika la Yehova.